Nathan Chikoya - Tiyenera Kukukondani текст песни

Все тексты песен Nathan Chikoya

Mwandivutikira pamtandapo kulibe wina monga inu.
Ndinyenera kukukwezani kulibe wina monga inu,
Ine ndi abale anga mwatikonzera njira, njira yabwino.
Tiyenera kukukondani, tiyenera kukukondani.
Tiyenera kukukondani, tiyenera kukukondani.


Kulibe wina monga inu Mulungu wathu, kulibe wina monga inu Ambuye Yesu.
Kulibe wina monga inu Mulungu wathu, kulibe wina monga inu Ambuye Yesu.
Tiyenera kukukondani, tiyenera kukukondani,
tiyenera kukukondani, tiyenera kukukondani.


Mawe mawe wavutika mwanawankosa chifukwa change ine.

Ume!! ume !mawe! mawe! Yesu wavutikiranji
Eli !Eli! akesa mwadzi wake chifukwa cha ine.

Wandiyeretsa wandipatsa moyo ndiyenera kukukondani,
Wandiyeretsa wandipatsa moyo ndiyenera kukukondani.


Kana ndiri naco chuma chadziko lapansi
Ndingacitaye chifukwa chachikondi chake chandipatsa moyo.
Ndinyadira pamtandapo pomwe anandifera Yesu
Mwini wamoyo kutaya moyo wake chifukwa chaine. (Anakesedwa mwadzi)


Chifukwa chaine, chifukwa chaine, chifukwa chaine, chifukwa chaine.


[Words and music by Nathan Chikoya
Written on 22nd February 07, recorded on 11th January 10
© 2010 Nathan Chikoya
Public Notice: All rights reserved.
Print only for musical research and church use.]

ДОБАВИТЬ ТЕКСТ В ЛИЧНЫЙ СПИСОК

Комментарии

Имя:
Сообщение:

Популярные тексты Nathan Chikoya

1 Praise God
2 Ndasaniya Moyo